Machitidwe 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zitatero anadumpha nʼkuimirira+ ndipo anayamba kuyenda. Iye analowa nawo limodzi mʼkachisimo, akuyenda, kudumphadumpha komanso kutamanda Mulungu.
8 Zitatero anadumpha nʼkuimirira+ ndipo anayamba kuyenda. Iye analowa nawo limodzi mʼkachisimo, akuyenda, kudumphadumpha komanso kutamanda Mulungu.