Machitidwe 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo anamuzindikira kuti ndi munthu amene ankakhala pa Geti Lokongola la kachisi+ nʼkumapempha mphatso zachifundo. Ndipo anthuwo anadabwa kwambiri ndi zimene zinamuchitikirazo.
10 Iwo anamuzindikira kuti ndi munthu amene ankakhala pa Geti Lokongola la kachisi+ nʼkumapempha mphatso zachifundo. Ndipo anthuwo anadabwa kwambiri ndi zimene zinamuchitikirazo.