Machitidwe 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma pamenepa Mulungu wakwaniritsa zimene analengezeratu kudzera mwa aneneri onse, kuti Khristu wake adzavutika.+
18 Koma pamenepa Mulungu wakwaniritsa zimene analengezeratu kudzera mwa aneneri onse, kuti Khristu wake adzavutika.+