Machitidwe 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipotu Mose ananena kuti, ‘Yehova* Mulungu wanu adzakupatsani mneneri ngati ine kuchokera pakati pa abale anu.+ Mudzamumvere pa zinthu zonse zimene adzakuuzeni.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:22 Nsanja ya Olonda,11/15/1991, ptsa. 28-31
22 Ndipotu Mose ananena kuti, ‘Yehova* Mulungu wanu adzakupatsani mneneri ngati ine kuchokera pakati pa abale anu.+ Mudzamumvere pa zinthu zonse zimene adzakuuzeni.+