Machitidwe 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho anawagwira nʼkuwatsekera mʼndende+ mpaka tsiku lotsatira, chifukwa kunali kutada kale.