Machitidwe 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Panalinso Anasi+ wansembe wamkulu, Kayafa,+ Yohane, Alekizanda ndiponso anthu onse omwe anali achibale a wansembe wamkuluyo. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:6 Nsanja ya Olonda,4/1/2012, tsa. 9
6 Panalinso Anasi+ wansembe wamkulu, Kayafa,+ Yohane, Alekizanda ndiponso anthu onse omwe anali achibale a wansembe wamkuluyo.