-
Machitidwe 4:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndiyeno anaimika Petulo ndi Yohane pakati pawo nʼkuyamba kuwafunsa kuti: “Kodi mphamvu zochitira zimenezi mwazitenga kuti, kapena mwachita izi mʼdzina la ndani?”
-