Machitidwe 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno popeza munthu wochiritsidwa uja anali ataimanso pomwepo,+ iwo anasowa chonena.+