Machitidwe 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 kuti: “Titani nawo anthu amenewa?+ Chifukwa kunena zoona, iwo achita chizindikiro chachikulu moti anthu onse a ku Yerusalemu aona.+ Ndipo ife sitingatsutse zimenezi.
16 kuti: “Titani nawo anthu amenewa?+ Chifukwa kunena zoona, iwo achita chizindikiro chachikulu moti anthu onse a ku Yerusalemu aona.+ Ndipo ife sitingatsutse zimenezi.