Machitidwe 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho kuti nkhaniyi isapitirire kufalikira kwa anthu ena, tiyeni tiwaopseze nʼkuwauza kuti asalankhulenso mʼdzina limeneli kwa munthu wina aliyense.”+
17 Choncho kuti nkhaniyi isapitirire kufalikira kwa anthu ena, tiyeni tiwaopseze nʼkuwauza kuti asalankhulenso mʼdzina limeneli kwa munthu wina aliyense.”+