Machitidwe 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho atawaopsezanso, anawamasula, popeza sanapeze chifukwa chilichonse chowapatsira chilango. Komanso ankaopa anthu,+ poti onse ankatamanda Mulungu chifukwa cha zimene zinachitikazo.
21 Choncho atawaopsezanso, anawamasula, popeza sanapeze chifukwa chilichonse chowapatsira chilango. Komanso ankaopa anthu,+ poti onse ankatamanda Mulungu chifukwa cha zimene zinachitikazo.