Machitidwe 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zimenezi zinachitikadi pamene Herode, Pontiyo Pilato,+ anthu a mitundu ina komanso anthu a mu Isiraeli, anasonkhana mumzindawu nʼkuukira Yesu, mtumiki wanu woyera, amene inu munamudzoza.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:27 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 23-24
27 Zimenezi zinachitikadi pamene Herode, Pontiyo Pilato,+ anthu a mitundu ina komanso anthu a mu Isiraeli, anasonkhana mumzindawu nʼkuukira Yesu, mtumiki wanu woyera, amene inu munamudzoza.+