Machitidwe 4:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Komanso, atumwiwo anapitiriza kuchitira umboni mwamphamvu kwambiri za kuuka kwa Ambuye Yesu.+ Ndipo Mulungu ankawasonyeza onsewo kukoma mtima kwakukulu.
33 Komanso, atumwiwo anapitiriza kuchitira umboni mwamphamvu kwambiri za kuuka kwa Ambuye Yesu.+ Ndipo Mulungu ankawasonyeza onsewo kukoma mtima kwakukulu.