Machitidwe 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho atumwi 12 aja anaitana gulu la ophunzira nʼkunena kuti: “Nʼzosayenera kuti ife tisiye ntchito yophunzitsa mawu a Mulungu nʼkuyamba kugawa chakudya.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:2 Nsanja ya Olonda,8/15/1994, tsa. 26
2 Choncho atumwi 12 aja anaitana gulu la ophunzira nʼkunena kuti: “Nʼzosayenera kuti ife tisiye ntchito yophunzitsa mawu a Mulungu nʼkuyamba kugawa chakudya.+