-
Machitidwe 6:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Zimenezi zinakwiyitsa kwambiri akulu, alembi ndiponso anthu ena. Ndiyeno anabwera modzidzimutsa nʼkumugwira ndipo anapita naye ku Khoti Lalikulu la Ayuda.
-