-
Machitidwe 6:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Anthu onse amene anali mʼbwalo la Khoti Lalikulu la Ayuda atayangʼanitsitsa Sitefano, anaona kuti nkhope yake ikuoneka ngati ya mngelo.
-