-
Machitidwe 8:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Anthu ambiri ankamvetsera zimene Filipo ankanena. Onse ankamvetsera ndiponso kuona zizindikiro zimene iye ankachita.
-