Machitidwe 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumeneko kunali anthu ambiri omwe anali ndi mizimu yoipa ndipo inkafuula nʼkutuluka.+ Anthu ambiri akufa ziwalo ndiponso olumala ankachiritsidwa.
7 Kumeneko kunali anthu ambiri omwe anali ndi mizimu yoipa ndipo inkafuula nʼkutuluka.+ Anthu ambiri akufa ziwalo ndiponso olumala ankachiritsidwa.