-
Machitidwe 8:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Mumzindawo munalinso munthu wina dzina lake Simoni. Izi zisanachitike, iye ankachita zamatsenga nʼkumadabwitsa anthu onse a ku Samariya ndipo ankadzitama kwambiri.
-