Machitidwe 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Simoni uja nayenso anakhala wokhulupirira. Atabatizidwa, sankasiyana ndi Filipo+ kulikonse. Moti ankadabwa poona zizindikiro ndiponso ntchito zamphamvu ndi zazikulu zomwe zinkachitika.
13 Simoni uja nayenso anakhala wokhulupirira. Atabatizidwa, sankasiyana ndi Filipo+ kulikonse. Moti ankadabwa poona zizindikiro ndiponso ntchito zamphamvu ndi zazikulu zomwe zinkachitika.