Machitidwe 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye ananena kuti: “Inenso mundipatseko mphamvu imeneyi, kuti aliyense amene ndingamugwire pamutu* azilandira mzimu woyera.”
19 Iye ananena kuti: “Inenso mundipatseko mphamvu imeneyi, kuti aliyense amene ndingamugwire pamutu* azilandira mzimu woyera.”