Machitidwe 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho lapa zoipa zimene wachitazi ndipo upemphe Yehova* mochonderera kuti ngati nʼkotheka, akukhululukire chifukwa cha maganizo oipa amene ali mumtima mwakowa.
22 Choncho lapa zoipa zimene wachitazi ndipo upemphe Yehova* mochonderera kuti ngati nʼkotheka, akukhululukire chifukwa cha maganizo oipa amene ali mumtima mwakowa.