Machitidwe 8:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho atamaliza kuchitira umboni mokwanira ndiponso kulankhula mawu a Yehova,* anabwerera ku Yerusalemu. Pobwerera ankalengeza uthenga wabwino mʼmidzi yambiri ya ku Samariya.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:25 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54
25 Choncho atamaliza kuchitira umboni mokwanira ndiponso kulankhula mawu a Yehova,* anabwerera ku Yerusalemu. Pobwerera ankalengeza uthenga wabwino mʼmidzi yambiri ya ku Samariya.+