-
Machitidwe 8:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Iye anayankha kuti: “Ndingamvetse bwanji popanda wondimasulira?” Choncho anapempha Filipo kuti akwere nʼkukhala naye mʼgaletamo.
-