Machitidwe 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mawu a mʼMalemba amene ankawerengawo anali akuti: “Anamutengera kumalo oti akamuphere ngati nkhosa. Ndipo mofanana ndi mwana wa nkhosa amene wangokhala chete pamene akufuna kumumeta ubweya, sanatsegule pakamwa pake.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:32 Nsanja ya Olonda,7/15/1996, tsa. 8
32 Mawu a mʼMalemba amene ankawerengawo anali akuti: “Anamutengera kumalo oti akamuphere ngati nkhosa. Ndipo mofanana ndi mwana wa nkhosa amene wangokhala chete pamene akufuna kumumeta ubweya, sanatsegule pakamwa pake.+