Machitidwe 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pamene ankamuchititsa manyazi, sanamuchitire zachilungamo.+ Ndi ndani angafotokoze mwatsatanetsatane mʼbadwo wa makolo ake? Chifukwa moyo wake wachotsedwa padziko lapansi.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:33 Nsanja ya Olonda,7/15/1996, tsa. 8
33 Pamene ankamuchititsa manyazi, sanamuchitire zachilungamo.+ Ndi ndani angafotokoze mwatsatanetsatane mʼbadwo wa makolo ake? Chifukwa moyo wake wachotsedwa padziko lapansi.”+