-
Machitidwe 8:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Ndiyeno ndunayo inafunsa Filipo kuti: “Ndiuzeni chonde, kodi mneneriyu akunena za ndani? Za iyeyo kapena za munthu wina?”
-