Machitidwe 8:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Atatuluka mʼmadzimo mzimu wa Yehova* unamuchotsapo Filipo mwamsanga ndipo nduna ija sinamuonenso, koma inapitiriza ulendo wake ikusangalala.
39 Atatuluka mʼmadzimo mzimu wa Yehova* unamuchotsapo Filipo mwamsanga ndipo nduna ija sinamuonenso, koma inapitiriza ulendo wake ikusangalala.