Machitidwe 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kukapempha makalata a chilolezo kuti apite nawo kumasunagoge a ku Damasiko. Anapempha makalatawo kuti akakapeza wina aliyense wotsatira Njirayo,*+ mwamuna kapena mkazi, akamumange nʼkubwera naye ku Yerusalemu. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:2 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 60-61 Nsanja ya Olonda,1/15/2000, tsa. 276/1/1990, tsa. 18
2 kukapempha makalata a chilolezo kuti apite nawo kumasunagoge a ku Damasiko. Anapempha makalatawo kuti akakapeza wina aliyense wotsatira Njirayo,*+ mwamuna kapena mkazi, akamumange nʼkubwera naye ku Yerusalemu.