Machitidwe 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu amene anali naye limodzi pa ulendowo, anangoima kusowa chonena. Iwo anamva ndithu kuti munthu akulankhula, koma sanaone aliyense.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:7 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 18
7 Anthu amene anali naye limodzi pa ulendowo, anangoima kusowa chonena. Iwo anamva ndithu kuti munthu akulankhula, koma sanaone aliyense.+