Machitidwe 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Ambuyewo anamuuza kuti: “Nyamuka upite ku Msewu Wowongoka. Ukakafika panyumba ya Yudasi, ukafunse za munthu wina dzina lake Saulo, wa ku Tariso.+ Iyeyo akupemphera, Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:11 Nsanja ya Olonda,9/15/2004, tsa. 321/15/2000, tsa. 28 Galamukani!,2/8/2003, ptsa. 28-30
11 Kenako Ambuyewo anamuuza kuti: “Nyamuka upite ku Msewu Wowongoka. Ukakafika panyumba ya Yudasi, ukafunse za munthu wina dzina lake Saulo, wa ku Tariso.+ Iyeyo akupemphera,