17 Choncho Hananiya anapita nʼkukalowa mʼnyumbamo. Ndiyeno anamugwira pamutu nʼkunena kuti: “Mʼbale wanga Saulo, Ambuye Yesu amene anaonekera kwa iwe pamsewu umene unadzera, wandituma. Wandituma kwa iwe kuti uyambenso kuona komanso udzazidwe ndi mzimu woyera.”+