Machitidwe 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atadya chakudya anapezanso mphamvu. Iye anakhala ndi ophunzira ku Damasiko kwa masiku angapo.+