Machitidwe 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho Baranaba+ anamuthandiza popita naye kwa atumwi. Ndipo anawafotokozera mwatsatanetsatane mmene Saulo anaonera Ambuye+ amene analankhula naye pamsewu. Anawafotokozeranso mmene Saulo analankhulira molimba mtima ku Damasiko mʼdzina la Yesu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:27 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 65 Nsanja ya Olonda,6/15/2007, ptsa. 15-164/15/1998, tsa. 21
27 Choncho Baranaba+ anamuthandiza popita naye kwa atumwi. Ndipo anawafotokozera mwatsatanetsatane mmene Saulo anaonera Ambuye+ amene analankhula naye pamsewu. Anawafotokozeranso mmene Saulo analankhulira molimba mtima ku Damasiko mʼdzina la Yesu.+