Machitidwe 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno mpingo ku Yudeya konse, ku Galileya ndi ku Samariya+ unayamba kukhala pamtendere ndipo unali wolimba. Chifukwa choti ophunzira ankaopa Yehova* komanso ankalimbikitsidwa ndi mzimu woyera,+ mpingowo unkakulirakulira. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:31 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 65-66 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2017, tsa. 13 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, tsa. 314/15/2007, tsa. 226/1/1990, tsa. 15
31 Ndiyeno mpingo ku Yudeya konse, ku Galileya ndi ku Samariya+ unayamba kukhala pamtendere ndipo unali wolimba. Chifukwa choti ophunzira ankaopa Yehova* komanso ankalimbikitsidwa ndi mzimu woyera,+ mpingowo unkakulirakulira.
9:31 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 65-66 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2017, tsa. 13 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, tsa. 314/15/2007, tsa. 226/1/1990, tsa. 15