Machitidwe 9:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndiyeno Petulo anamuuza kuti: “Eneya, Yesu Khristu akukuchiritsa.+ Dzuka ndipo ukonze pabedi lakolo.”+ Nthawi yomweyo anadzuka.
34 Ndiyeno Petulo anamuuza kuti: “Eneya, Yesu Khristu akukuchiritsa.+ Dzuka ndipo ukonze pabedi lakolo.”+ Nthawi yomweyo anadzuka.