Machitidwe 9:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Petulo anamugwira dzanja nʼkumuimiritsa. Atatero anaitana oyerawo komanso akazi amasiye aja, ndipo onse anaona kuti Tabita ali moyo.+
41 Petulo anamugwira dzanja nʼkumuimiritsa. Atatero anaitana oyerawo komanso akazi amasiye aja, ndipo onse anaona kuti Tabita ali moyo.+