-
Machitidwe 10:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Iyeyu ankakonda zopemphera ndipo ankaopa Mulungu pamodzi ndi banja lake lonse. Komanso ankapatsa anthu mphatso zachifundo zambiri ndipo ankapemphera mochonderera kwa Mulungu nthawi zonse.
-