Machitidwe 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zitatero, Koneliyo anayangʼanitsitsa mngeloyo mwamantha nʼkunena kuti: “Lankhulani Mbuyanga.” Mngeloyo anamuuza kuti: “Mulungu wamva mapemphero ako ndiponso waona mphatso zako zachifundo.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:4 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, ptsa. 18-191/15/1990, tsa. 6
4 Zitatero, Koneliyo anayangʼanitsitsa mngeloyo mwamantha nʼkunena kuti: “Lankhulani Mbuyanga.” Mngeloyo anamuuza kuti: “Mulungu wamva mapemphero ako ndiponso waona mphatso zako zachifundo.+