-
Machitidwe 10:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mʼmasomphenyawo anaona kumwamba kutatseguka, chinthu chinachake chooneka ngati chinsalu chachikulu chikutsika. Chinthucho anachigwira mʼmakona onse 4 nʼkumachitsitsira padziko lapansi.
-