Machitidwe 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Petulo atathedwa nzeru chifukwa chosamvetsa tanthauzo la masomphenyawo, anthu amene Koneliyo anawatuma aja anafunsa kuti nyumba ya Simoni ili kuti ndipo anali ataima pageti.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:17 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 71
17 Petulo atathedwa nzeru chifukwa chosamvetsa tanthauzo la masomphenyawo, anthu amene Koneliyo anawatuma aja anafunsa kuti nyumba ya Simoni ili kuti ndipo anali ataima pageti.+