Machitidwe 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Petulo akuganizirabe za masomphenyawo, mzimu wa Mulungu+ unamuuza kuti: “Petulo! Pali anthu atatu amene akukufuna.
19 Petulo akuganizirabe za masomphenyawo, mzimu wa Mulungu+ unamuuza kuti: “Petulo! Pali anthu atatu amene akukufuna.