-
Machitidwe 10:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Tsiku lotsatira anafika ku Kaisareya ndipo Koneliyo ankawayembekezeradi. Iye anali atasonkhanitsa achibale ake ndi anzake apamtima.
-