Machitidwe 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho tumiza anthu ku Yopa kuti akaitane Simoni wotchedwanso Petulo. Munthu ameneyo ndi mlendo mʼnyumba ya Simoni wofufuta zikopa, amene amakhala mʼmbali mwa nyanja.’+
32 Choncho tumiza anthu ku Yopa kuti akaitane Simoni wotchedwanso Petulo. Munthu ameneyo ndi mlendo mʼnyumba ya Simoni wofufuta zikopa, amene amakhala mʼmbali mwa nyanja.’+