Machitidwe 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Nthawi yomweyo ndinatuma anthu kuti akakuitaneni ndipo mwatikomera mtima nʼkubwera. Choncho tonse tili pano pamaso pa Mulungu, kuti timve zonse zimene Yehova* wakulamulani kuti mutiuze.”
33 Nthawi yomweyo ndinatuma anthu kuti akakuitaneni ndipo mwatikomera mtima nʼkubwera. Choncho tonse tili pano pamaso pa Mulungu, kuti timve zonse zimene Yehova* wakulamulani kuti mutiuze.”