Machitidwe 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Nkhani yake inali yonena za Yesu wa ku Nazareti, amene Mulungu anamudzoza ndi mzimu woyera+ ndi mphamvu. Popeza Mulungu anali naye,+ anayenda mʼdziko lonse nʼkumachita zabwino ndiponso kuchiritsa anthu onse amene Mdyerekezi+ ankawazunza. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:38 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2020, tsa. 31 Nkhani za M’Baibulo, ptsa. 186-187
38 Nkhani yake inali yonena za Yesu wa ku Nazareti, amene Mulungu anamudzoza ndi mzimu woyera+ ndi mphamvu. Popeza Mulungu anali naye,+ anayenda mʼdziko lonse nʼkumachita zabwino ndiponso kuchiritsa anthu onse amene Mdyerekezi+ ankawazunza.