-
Machitidwe 10:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Ndipo ife ndife mboni za zinthu zonse zimene anachita mʼdziko la Ayuda ndi ku Yerusalemu komwe. Koma Aisiraeliwo anamupha pomupachika pamtengo.
-