Machitidwe 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atafika kumeneko nʼkuona kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, anasangalala ndipo anayamba kulimbikitsa onse kuti apitirize ndi mtima wonse kukhala okhulupirika kwa Ambuye.+
23 Atafika kumeneko nʼkuona kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, anasangalala ndipo anayamba kulimbikitsa onse kuti apitirize ndi mtima wonse kukhala okhulupirika kwa Ambuye.+