Machitidwe 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho ophunzirawo anatsimikiza mtima kutumiza thandizo+ kwa abale a ku Yudeya, aliyense mogwirizana ndi zimene akanakwanitsa.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:29 Nsanja ya Olonda,4/15/1998, tsa. 21
29 Choncho ophunzirawo anatsimikiza mtima kutumiza thandizo+ kwa abale a ku Yudeya, aliyense mogwirizana ndi zimene akanakwanitsa.+