Machitidwe 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anamugwira nʼkumutsekera mʼndende+ ndipo anamusiya mʼmanja mwa magulu 4 a asilikali kuti azisinthana pomulondera. Gulu lililonse linali ndi asilikali 4. Cholinga cha Herode chinali chakuti adzamuzenge mlandu pamaso pa anthu Pasika akatha. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:4 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 77-78 Nsanja ya Olonda,1/15/2012, tsa. 116/1/1990, tsa. 20
4 Anamugwira nʼkumutsekera mʼndende+ ndipo anamusiya mʼmanja mwa magulu 4 a asilikali kuti azisinthana pomulondera. Gulu lililonse linali ndi asilikali 4. Cholinga cha Herode chinali chakuti adzamuzenge mlandu pamaso pa anthu Pasika akatha.